-
Machitidwe 28:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Anthu olankhula chilankhulo chachilendo kumeneko anatisonyeza kukoma mtima kwapadera. Iwo anasonkha moto nʼkutilandira bwino tonse chifukwa kunkagwa mvula ndiponso kunkazizira.
-