-
Machitidwe 28:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Anthuwo ankayembekezera kuti atupa kapena agwa mwadzidzidzi nʼkufa. Koma atayembekezera kwa nthawi yaitali nʼkuona kuti palibe chimene chikumuchitikira, anasintha maganizo nʼkuyamba kunena kuti ndi mulungu.
-