Machitidwe 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Abale akumeneko atamva za ife, anabwera mpaka kudzafika ku Msika wa Apiyo ndi ku Nyumba Zitatu za Alendo kudzatichingamira. Paulo atawaona, anathokoza Mulungu ndipo analimba mtima.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:15 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 212-213 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2020, ptsa. 16-17 Nsanja ya Olonda,1/1/2010, tsa. 1110/15/2006, ptsa. 14, 16-1712/15/2004, ptsa. 16-17
15 Abale akumeneko atamva za ife, anabwera mpaka kudzafika ku Msika wa Apiyo ndi ku Nyumba Zitatu za Alendo kudzatichingamira. Paulo atawaona, anathokoza Mulungu ndipo analimba mtima.+
28:15 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 212-213 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2020, ptsa. 16-17 Nsanja ya Olonda,1/1/2010, tsa. 1110/15/2006, ptsa. 14, 16-1712/15/2004, ptsa. 16-17