Machitidwe 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Ayuda anatsutsa zimenezo moti ndinakakamizika kupempha kudzaonekera kwa Kaisara.+ Komatu sikuti ndinachita zimenezi chifukwa choti ndinkafuna kudzaneneza mtundu wanga. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:19 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 213-214
19 Koma Ayuda anatsutsa zimenezo moti ndinakakamizika kupempha kudzaonekera kwa Kaisara.+ Komatu sikuti ndinachita zimenezi chifukwa choti ndinkafuna kudzaneneza mtundu wanga.