Machitidwe 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa chifukwa chimenechi, ndinapempha kuti ndidzaonane nanu nʼkulankhula nanu, popeza ndamangidwa ndi unyolo uwu chifukwa cha chiyembekezo cha Aisiraeli.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:20 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 214
20 Pa chifukwa chimenechi, ndinapempha kuti ndidzaonane nanu nʼkulankhula nanu, popeza ndamangidwa ndi unyolo uwu chifukwa cha chiyembekezo cha Aisiraeli.”+