-
Machitidwe 28:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Zitatero anapangana tsiku loti adzakumane naye ndipo anabweradi ambiri kumene iye ankakhala. Choncho kuyambira mʼmawa mpaka madzulo, anawafotokozera nkhani yonse ndipo anachitira umboni mokwanira za Ufumu wa Mulungu. Anachita zimenezi pogwiritsa ntchito mfundo zokopa zokhudza Yesu,+ kuchokera mʼChilamulo cha Mose+ ndi zimene aneneri analemba.+
-