Aroma 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kudzera mwa iyeyu, Mulungu anatisonyeza kukoma mtima kwakukulu ndipo ndinasankhidwa kukhala mtumwi+ kuti ndikathandize anthu a mitundu yonse kuti asonyeze chikhulupiriro, akhale omvera+ ndiponso kuti alemekeze dzina lake.
5 Kudzera mwa iyeyu, Mulungu anatisonyeza kukoma mtima kwakukulu ndipo ndinasankhidwa kukhala mtumwi+ kuti ndikathandize anthu a mitundu yonse kuti asonyeze chikhulupiriro, akhale omvera+ ndiponso kuti alemekeze dzina lake.