Aroma 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nthawi zonse ndikamapemphera ndimakutchulani mʼmapemphero anga ndipo Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika ndi mtima wanga wonse polalikira uthenga wabwino wonena za Mwana wake, akundichitira umboni.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Nsanja ya Olonda,11/15/2000, tsa. 12
9 Nthawi zonse ndikamapemphera ndimakutchulani mʼmapemphero anga ndipo Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika ndi mtima wanga wonse polalikira uthenga wabwino wonena za Mwana wake, akundichitira umboni.+