-
Aroma 1:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma abale ndikufuna mudziwe kuti kwa nthawi yaitali ndakhala ndikufuna kubwera kwanuko, koma zakhala zikulephereka. Ndikufuna ndidzaone zotsatira zabwino za ntchito yathu yolalikira ngati mmene zilili pakati pa anthu a mitundu ina yonse.
-