Aroma 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ine sindichita manyazi ndi uthenga wabwino.+ Kunena zoona, uthengawo ndi njira yamphamvu imene Mulungu akuigwiritsa ntchito pofuna kupulumutsa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba Ayuda+ kenako Agiriki.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:16 Utumiki wa Ufumu,12/1995, Nsanja ya Olonda,1/1/1990, ptsa. 10-152/1/1987, tsa. 23
16 Ine sindichita manyazi ndi uthenga wabwino.+ Kunena zoona, uthengawo ndi njira yamphamvu imene Mulungu akuigwiritsa ntchito pofuna kupulumutsa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba Ayuda+ kenako Agiriki.+