-
Aroma 1:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Choncho mogwirizana ndi zilakolako zamʼmitima mwawo, Mulungu anawasiya kuti achite zonyansa, kuti achite zochititsa manyazi ndi matupi awo.
-