Aroma 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Popeza sankaona kuti nʼzofunika kudziwa Mulungu molondola, iye anawasiya kuti apitirize kuganiza zoipa nʼkumachita zinthu zosayenera.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:28 Nsanja ya Olonda,12/1/1989, ptsa. 10-11 Galamukani!,7/8/1989, ptsa. 30-31
28 Popeza sankaona kuti nʼzofunika kudziwa Mulungu molondola, iye anawasiya kuti apitirize kuganiza zoipa nʼkumachita zinthu zosayenera.+