Aroma 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndipo ankachita zosalungama za mtundu ulionse,+ kuipa konse, dyera*+ ndiponso zinthu zonse zoipa. Mtima wawo unadzaza ndi kaduka,+ kupha anthu,+ ndewu, chinyengo+ ndi njiru.+ Ankakondanso miseche
29 Ndipo ankachita zosalungama za mtundu ulionse,+ kuipa konse, dyera*+ ndiponso zinthu zonse zoipa. Mtima wawo unadzaza ndi kaduka,+ kupha anthu,+ ndewu, chinyengo+ ndi njiru.+ Ankakondanso miseche