Aroma 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngakhale kuti anthuwa amalidziwa bwino lamulo lolungama la Mulungu, lakuti amene amachita zinthu zimenezi ndi oyenera imfa,+ amapitiriza kuzichita. Kuwonjezera pamenepo, amagwirizananso ndi anthu amene amachita zimenezi.
32 Ngakhale kuti anthuwa amalidziwa bwino lamulo lolungama la Mulungu, lakuti amene amachita zinthu zimenezi ndi oyenera imfa,+ amapitiriza kuzichita. Kuwonjezera pamenepo, amagwirizananso ndi anthu amene amachita zimenezi.