Aroma 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho kaya ndiwe ndani,+ ngati umaweruza ena, ulibe chifukwa chomveka chodzilungamitsira. Popeza ukamaweruza ena, umakhala ukudzitsutsa wekha, chifukwa iwenso umachita zomwezo.+
2 Choncho kaya ndiwe ndani,+ ngati umaweruza ena, ulibe chifukwa chomveka chodzilungamitsira. Popeza ukamaweruza ena, umakhala ukudzitsutsa wekha, chifukwa iwenso umachita zomwezo.+