Aroma 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Adzapereka moyo wosatha kwa anthu amene akupitirizabe kuchita zabwino.+ Anthu amenewa akuyesetsa kupeza ulemerero, ulemu ndi moyo wosawonongeka.
7 Adzapereka moyo wosatha kwa anthu amene akupitirizabe kuchita zabwino.+ Anthu amenewa akuyesetsa kupeza ulemerero, ulemu ndi moyo wosawonongeka.