Aroma 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma anthu amene amakonda mikangano, satsatira choonadi komanso amachita zosalungama, Mulungu adzawasonyeza mkwiyo wake.+
8 Koma anthu amene amakonda mikangano, satsatira choonadi komanso amachita zosalungama, Mulungu adzawasonyeza mkwiyo wake.+