Aroma 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu a mitundu ina alibe Chilamulo.+ Koma akamachita mwachibadwa zinthu zomwe zili mʼChilamulo, ngakhale kuti alibe Chilamulo, amasonyeza kuti ali ndi Chilamulo mumtima mwawo. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:14 Nsanja ya Olonda,10/15/2007, ptsa. 20-2110/1/2005, tsa. 125/1/2000, tsa. 165/1/1996, tsa. 15
14 Anthu a mitundu ina alibe Chilamulo.+ Koma akamachita mwachibadwa zinthu zomwe zili mʼChilamulo, ngakhale kuti alibe Chilamulo, amasonyeza kuti ali ndi Chilamulo mumtima mwawo.