-
Aroma 2:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Amenewa amasonyeza kuti mfundo za mʼChilamulo zinalembedwa mʼmitima mwawo ndipo chikumbumtima chawo chimawachitira umboni. Anthu amenewa maganizo awo amawatsutsa kapenanso kuwavomereza.
-