Aroma 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mumadziwa zimene Mulungu amafuna komanso mumasangalala ndi zinthu zabwino kwambiri chifukwa chakuti munaphunzitsidwa Chilamulo.+
18 Mumadziwa zimene Mulungu amafuna komanso mumasangalala ndi zinthu zabwino kwambiri chifukwa chakuti munaphunzitsidwa Chilamulo.+