Aroma 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi iwe amene umaphunzitsa ena, bwanji sudziphunzitsa wekha?+ Umalalikira kuti, “Usabe,”+ ndiye iwe umabanso? Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:21 Nsanja ya Olonda,6/15/2002, ptsa. 17-22
21 Kodi iwe amene umaphunzitsa ena, bwanji sudziphunzitsa wekha?+ Umalalikira kuti, “Usabe,”+ ndiye iwe umabanso?