Aroma 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ayi. Ngakhale munthu aliyense atakhala wabodza,+ Mulungu angapezekebe kuti ndi wonena zoona+ mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Mukamalankhula, mumalankhula zachilungamo kuti muwine pamene mukuweruzidwa.”+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:4 Nsanja ya Olonda,6/15/2008, tsa. 30
4 Ayi. Ngakhale munthu aliyense atakhala wabodza,+ Mulungu angapezekebe kuti ndi wonena zoona+ mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Mukamalankhula, mumalankhula zachilungamo kuti muwine pamene mukuweruzidwa.”+