-
Aroma 3:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Komabe ngati kusalungama kwathu kukusonyeza bwino kuti Mulungu ndi wolungama, ndiye tinene kuti chiyani? Kodi tingati Mulungu ndi wosalungama akamaonetsa mkwiyo wake? (Ndikulankhula ngati mmene anthu ena amalankhulira.)
-