Aroma 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndilekerenji kunena zimene ena amatinamizira kuti timanena zija, zakuti: “Tiyeni tichite zoipa kuti pakhale zinthu zabwino”? Anthu amene amanena zimenezi adzaweruzidwa mogwirizana ndi chilungamo.+
8 Ndilekerenji kunena zimene ena amatinamizira kuti timanena zija, zakuti: “Tiyeni tichite zoipa kuti pakhale zinthu zabwino”? Anthu amene amanena zimenezi adzaweruzidwa mogwirizana ndi chilungamo.+