Aroma 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiye kodi zikatero Ayudafe tili pabwino kuposa ena? Ayi ndithu. Chifukwa monga tanena kale, Ayuda ndiponso Agiriki, onse amalamuliridwa ndi uchimo+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Nsanja ya Olonda,12/1/1997, tsa. 11
9 Ndiye kodi zikatero Ayudafe tili pabwino kuposa ena? Ayi ndithu. Chifukwa monga tanena kale, Ayuda ndiponso Agiriki, onse amalamuliridwa ndi uchimo+