Aroma 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu onse apatuka, ndipo onse akhala opanda pake. Palibiretu ndi mmodzi yemwe amene akusonyeza kukoma mtima.”+
12 Anthu onse apatuka, ndipo onse akhala opanda pake. Palibiretu ndi mmodzi yemwe amene akusonyeza kukoma mtima.”+