Aroma 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mulungu anamupereka ngati nsembe yoti anthu agwirizanenso ndi Mulunguyo+ pokhulupirira magazi ake.+ Anachita zimenezi pofuna kuonetsa chilungamo chake chifukwa anasonyeza kuti ndi wosakwiya msanga pokhululuka machimo amene anachitika kale. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:25 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2024, tsa. 32 Nsanja ya Olonda,8/15/2014, tsa. 188/15/2010, ptsa. 6-76/15/2008, tsa. 2911/1/2005, tsa. 132/15/1991, tsa. 18
25 Mulungu anamupereka ngati nsembe yoti anthu agwirizanenso ndi Mulunguyo+ pokhulupirira magazi ake.+ Anachita zimenezi pofuna kuonetsa chilungamo chake chifukwa anasonyeza kuti ndi wosakwiya msanga pokhululuka machimo amene anachitika kale.
3:25 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2024, tsa. 32 Nsanja ya Olonda,8/15/2014, tsa. 188/15/2010, ptsa. 6-76/15/2008, tsa. 2911/1/2005, tsa. 132/15/1991, tsa. 18