Aroma 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anachita zimenezi kuti asonyeze chilungamo chake+ pa nthawi inoyo poona kuti munthu amene amakhulupirira Yesu ndi wolungama.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:26 Nsanja ya Olonda,11/1/2005, tsa. 13
26 Anachita zimenezi kuti asonyeze chilungamo chake+ pa nthawi inoyo poona kuti munthu amene amakhulupirira Yesu ndi wolungama.+