-
Aroma 4:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Koma kodi iye anali wotani pamene anaonedwa kuti ndi wolungama? Kodi anali wodulidwa kapena wosadulidwa? Iyetu anali asanadulidwe.
-