Aroma 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zoona zake nʼzakuti, kuphwanya Chilamulo kumachititsa kuti munthu alandire chilango,+ koma pamene palibe lamulo, palibenso kulakwa.+
15 Zoona zake nʼzakuti, kuphwanya Chilamulo kumachititsa kuti munthu alandire chilango,+ koma pamene palibe lamulo, palibenso kulakwa.+