Aroma 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, ankaganizira za thupi lake, limene pa nthawiyo linali ngati lakufa (popeza anali ndi zaka pafupifupi 100).+ Ankadziwanso kuti Sara ndi wokalamba kwambiri ndipo sangabereke mwana.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:19 Nsanja ya Olonda,7/1/2001, tsa. 21
19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, ankaganizira za thupi lake, limene pa nthawiyo linali ngati lakufa (popeza anali ndi zaka pafupifupi 100).+ Ankadziwanso kuti Sara ndi wokalamba kwambiri ndipo sangabereke mwana.+