-
Aroma 4:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma chifukwa cha lonjezo la Mulungu, chikhulupiriro chake sichinagwedezeke ndipo chikhulupiriro chakecho chinamupatsa mphamvu moti anapereka ulemerero kwa Mulungu.
-