Aroma 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kukhulupirira Yesu kumatithandiza kuti tizitha kufika kwa Mulungu komanso tizisangalala ndi kukoma mtima kwake kwakukulu.+ Ndipo tingathe kusangalala* chifukwa tili ndi chiyembekezo cholandira ulemerero wa Mulungu. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2023, ptsa. 9-10 Galamukani!,7/8/1999, tsa. 27
2 Kukhulupirira Yesu kumatithandiza kuti tizitha kufika kwa Mulungu komanso tizisangalala ndi kukoma mtima kwake kwakukulu.+ Ndipo tingathe kusangalala* chifukwa tili ndi chiyembekezo cholandira ulemerero wa Mulungu.