Aroma 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiponso adzachita zoposa pamenepo potipulumutsa ku mkwiyo wake kudzera mwa Khristu,+ popeza tikuonedwa olungama chifukwa cha magazi a Khristuyo.+
9 Ndiponso adzachita zoposa pamenepo potipulumutsa ku mkwiyo wake kudzera mwa Khristu,+ popeza tikuonedwa olungama chifukwa cha magazi a Khristuyo.+