Aroma 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo si zokhazo, koma tikusangalalanso chifukwa cha ubwenzi wathu ndi Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, amene tagwirizanitsidwa ndi Mulungu kudzera mwa iye.+
11 Ndipo si zokhazo, koma tikusangalalanso chifukwa cha ubwenzi wathu ndi Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, amene tagwirizanitsidwa ndi Mulungu kudzera mwa iye.+