Aroma 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chilamulo chisanabwere, uchimo unalipo kale mʼdziko, koma munthu sangapezedwe ndi mlandu woti wachita tchimo ngati palibe lamulo.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:13 Nsanja ya Olonda,6/15/2011, tsa. 12
13 Chilamulo chisanabwere, uchimo unalipo kale mʼdziko, koma munthu sangapezedwe ndi mlandu woti wachita tchimo ngati palibe lamulo.+