Aroma 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Popeza kusamvera kwa munthu mmodziyo kunachititsa kuti ambiri akhale ochimwa,+ kumvera kwa munthu mmodziyu kudzachititsanso kuti ambiri akhale olungama.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:19 Nsanja ya Olonda,4/15/1999, tsa. 12
19 Popeza kusamvera kwa munthu mmodziyo kunachititsa kuti ambiri akhale ochimwa,+ kumvera kwa munthu mmodziyu kudzachititsanso kuti ambiri akhale olungama.+