Aroma 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chilamulo chinaperekedwa kuti kuchimwa kwa anthu kuonekere.+ Koma pamene uchimo unaonekera, kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu kunawonjezekanso kwambiri.
20 Chilamulo chinaperekedwa kuti kuchimwa kwa anthu kuonekere.+ Koma pamene uchimo unaonekera, kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu kunawonjezekanso kwambiri.