Aroma 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa tikudziwa kuti umunthu wathu wakale unapachikidwa naye+ limodzi pamtengo nʼcholinga chakuti thupi lathu lauchimo likhale lopanda mphamvu,+ kuti tisakhalenso akapolo a uchimo.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:6 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2022, tsa. 6
6 Chifukwa tikudziwa kuti umunthu wathu wakale unapachikidwa naye+ limodzi pamtengo nʼcholinga chakuti thupi lathu lauchimo likhale lopanda mphamvu,+ kuti tisakhalenso akapolo a uchimo.+