Aroma 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi simukudziwa kuti mukamadzipereka kwa winawake ngati akapolo omvera, mumakhala akapolo a amene mukumumverayo?+ Mumakhala akapolo a uchimo+ umene umatsogolera ku imfa,+ kapena akapolo a kumvera komwe kumatsogolera ku chilungamo. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:16 Nsanja ya Olonda,3/15/1998, ptsa. 15-17
16 Kodi simukudziwa kuti mukamadzipereka kwa winawake ngati akapolo omvera, mumakhala akapolo a amene mukumumverayo?+ Mumakhala akapolo a uchimo+ umene umatsogolera ku imfa,+ kapena akapolo a kumvera komwe kumatsogolera ku chilungamo.