Aroma 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inde, popeza munamasulidwa ku uchimo,+ munakhala akapolo a chilungamo.+