Aroma 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwachitsanzo, mkazi wokwatiwa amakhala womangidwa kwa mwamuna wake mwalamulo pamene mwamunayo ali moyo. Koma mwamunayo akamwalira, mkazi amakhala womasuka ku lamulo lokhudza mwamuna wake.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:2 Nsanja ya Olonda,2/15/2007, ptsa. 18-19
2 Mwachitsanzo, mkazi wokwatiwa amakhala womangidwa kwa mwamuna wake mwalamulo pamene mwamunayo ali moyo. Koma mwamunayo akamwalira, mkazi amakhala womasuka ku lamulo lokhudza mwamuna wake.+