Aroma 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa pamene tinkakhala mogwirizana ndi matupi athu ochimwawa, Chilamulo chinachititsa kuti zilakolako za uchimo zimene tinali nazo mʼmatupi* mwathu zionekere. Ndipo zilakolako zimenezi zikanatibweretsera imfa.+
5 Chifukwa pamene tinkakhala mogwirizana ndi matupi athu ochimwawa, Chilamulo chinachititsa kuti zilakolako za uchimo zimene tinali nazo mʼmatupi* mwathu zionekere. Ndipo zilakolako zimenezi zikanatibweretsera imfa.+