Aroma 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma chifukwa cha lamulo, uchimo unapeza njira yondichititsa kukhala ndi kusirira kwansanje kwa mtundu uliwonse. Chifukwa popanda Chilamulo, uchimo unali wopanda mphamvu.*+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:8 Nsanja ya Olonda,6/15/2008, tsa. 30
8 Koma chifukwa cha lamulo, uchimo unapeza njira yondichititsa kukhala ndi kusirira kwansanje kwa mtundu uliwonse. Chifukwa popanda Chilamulo, uchimo unali wopanda mphamvu.*+