Aroma 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mulungu adzandipulumutsa kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu. Choncho mʼmaganizo mwanga ndine kapolo wa malamulo a Mulungu, koma mʼthupi langa ndine kapolo wa lamulo la uchimo.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:25 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2017, tsa. 12 Nsanja ya Olonda,12/1/1997, tsa. 11
25 Mulungu adzandipulumutsa kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu. Choncho mʼmaganizo mwanga ndine kapolo wa malamulo a Mulungu, koma mʼthupi langa ndine kapolo wa lamulo la uchimo.+