3 Chilamulo chinalibe mphamvu yokumasulani+ chifukwa anthu ndi ofooka+ komanso ochimwa. Koma kuti akumasuleni, Mulungu anatumiza Mwana wake+ ali ndi thupi ngati la anthu ochimwa+ kuti athane ndi uchimo. Choncho Mulungu anagonjetsa uchimo pogwiritsa ntchito thupi.