Aroma 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komabe inu mukutsatira mzimu osati zofuna za thupi,+ ngati mzimu wa Mulungu ulidi ndi inu. Ngati wina alibe mzimu wa Khristu, ameneyu si wa Khristu.
9 Komabe inu mukutsatira mzimu osati zofuna za thupi,+ ngati mzimu wa Mulungu ulidi ndi inu. Ngati wina alibe mzimu wa Khristu, ameneyu si wa Khristu.