Aroma 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndikuona kuti mavuto amene tikukumana nawo panopa ndi aangʼono powayerekezera ndi ulemerero umene udzaonekere kudzera mwa ife.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:18 Nsanja ya Olonda,5/1/1999, ptsa. 4-5
18 Ndikuona kuti mavuto amene tikukumana nawo panopa ndi aangʼono powayerekezera ndi ulemerero umene udzaonekere kudzera mwa ife.+