-
Aroma 8:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Chifukwa tinapulumutsidwa tili ndi chiyembekezo chimenechi, koma chimene ukuchiyembekezera chikatheka sichikhalanso chiyembekezo. Kodi chimene munthu ankachiyembekezera chikachitika, amachiyembekezerabe?
-