-
Aroma 9:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndikunena zoona mogwirizana ndi Khristu, sindikunama ayi. Ndipo chikumbumtima changa chikundichitira umboni mwa mzimu woyera,
-